Gjoe roofing contractor

Gjoe roofing contractor Special list in different wooden materials and roofing

Tingokumbutsananapo pamene tangochilowa chakachi tiyeni timuyamike namalenga  watikondera ambili sanalowe nawo pano Ali ...
05/01/2023

Tingokumbutsananapo pamene tangochilowa chakachi tiyeni timuyamike namalenga watikondera ambili sanalowe nawo pano Ali ku Manda anamwalira

Create an account or log in to Facebook. Connect with friends, family and other people you know. Share photos and videos, send messages and get updates.

Posachedwapa takhoma nyumba ina pa chileka p***a apa timakhala osangalala ngati ma big mukamatipatsa job ngati izi
07/10/2022

Posachedwapa takhoma nyumba ina pa chileka p***a apa timakhala osangalala ngati ma big mukamatipatsa job ngati izi

Timathanso kupanga zinthu ngati izi komanso timapenta manyumba ngakhalenso kukhoma kanyumba kabwino ka alonda apa gate
24/08/2022

Timathanso kupanga zinthu ngati izi komanso timapenta manyumba ngakhalenso kukhoma kanyumba kabwino ka alonda apa gate

17/06/2022

Ulemu kwa mabwana nonsense ,ngati munamanga nyumba yoti denga lake lidzakhala la ngomi mutsatila malamulo awa: mudamanga nyumba yanu mwafika pa ringbeam level kuntundaku kukhale makozesi osachepela 8 komanso ngati abuilder Anu zakudziwa bwino Malo oyika wire ndiyekuti kuti gavanized wire yo asayike ife ngati akatswili pa nkhani ya madenge mwamaliza kumanga muyeneranso kukhale ndi quotation mukhale mukudziwa kuti nyumba yangayi idzafuna matabwa angati komanso misomali yochuluka bwanji ndi zinazofunika

30/05/2022

Ndikutha kudziwa kuti anthu ambiri akukolora mtedza (nsawa) koma chonde musayanike mtedza wanu padenga la malata muwononga malata ndipo malatawo kukadzabwera mvula mudzangodziwilatu kuti denga lanu latha ndipo malata Anu adzachitika ngati sefa amabowoka bowoka ngati kuti munthu anachita kukwerapo ndikumabowola ndi misomali ngakhale malata ake atakhala ma i b r adzabowokabe coz mumtedza muli sulphate amene amachokera mmakoko amtedzawo chonde uthengawu ugwilitseni ntchito kuti malata anuwo muzakhale nawo nthawi yayitali

Zikuoneka kuti aliyense wayambano kupanga budget yodziwika.moti mmene wafikila soya mtengowake  ili bwino koma osayiwala...
29/04/2022

Zikuoneka kuti aliyense wayambano kupanga budget yodziwika.moti mmene wafikila soya mtengowake ili bwino koma osayiwala kuguoiratu feteleza koma kuthamangila kukamwa kachasu tapanganizoti musinthikeko anthu ayambeko kumakulozelanani muli ndi njinga yabwino nyumba yabwino komanso umoyo wabwino enanu tikukhomeleni nyumba za ngomi mudamanga ifenso tikudalira za soya zomwezo

28/04/2022

Ndalama za soya zisatipengetse abale

28/03/2022

Abale tamuona soya wanu mmaminda yanu yesetsani kusamala ndalama zomwe mutapeze ndipo mukatero mukhoza kutukuka mosavuta osati kungozimwera mowa kumeneko ndikuchedwa

Ndife omwe aja timatha nkhani za madenga palibenso mundifufuze pa nkhani imeneyi anthu akuuzani
08/03/2022

Ndife omwe aja timatha nkhani za madenga palibenso mundifufuze pa nkhani imeneyi anthu akuuzani

Kodi mabwana mvula ndiye ikumagwa bwino in mukuona bwanji Chaka Chino kuli zokoloratu mwina tingananare
28/02/2022

Kodi mabwana mvula ndiye ikumagwa bwino in mukuona bwanji Chaka Chino kuli zokoloratu mwina tingananare

24/02/2022

Address

G Chiotha , P, O, Box 152, Namitete Lilongwe
Lilongwe

Opening Hours

09:00 - 17:00

Telephone

+265881567891

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Gjoe roofing contractor posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Gjoe roofing contractor:

Share