Madalitso kazombo kamatcheni

Madalitso kazombo kamatcheni Home grown attitude

26/11/2025

300 bags of maize available at Dedza Boma.
Price: K63,000
Contact: +265999963398

02/11/2025

Nkhondo yaku Tanzania yapangitsa kuti madzi ampopi asiye kutuluka kwa masiku atatu m'malawi muno.

01/11/2025

Tidikire APM akalumbira zinthu zikhala bwino πŸ˜†πŸ˜†.

Akangolumbira mafuta agalimoto akhala ngambwingambwi komaso otchipa.

Zinthu mu shop zikhala zochipa kwambiri.

Fertilizer akhala ngambwingambwi.

ku Malawi nkokoma kwambiri sindidzasamuka πŸ˜†πŸ˜†πŸ€ΈπŸ€Έ

26/10/2025

nde pali ziathuzina. zinvekele. bola mcp inachoka. komamuntima. zikulila usiku ndi usana. kuti ndinkayesanji ine.

13/10/2025

zamageti amathana nazo ndi chakwela yekha basi

waona zoti amachemelela zigawenga wangoganiza zozisiya za ndalezi bakili muluzi
10/10/2025

waona zoti amachemelela zigawenga wangoganiza zozisiya za ndalezi bakili muluzi

ine pheee
10/10/2025

ine pheee

10/10/2025

di pwii pwiii ikuphani anthu anga

Address

M1
Lilongwe

Telephone

+265881652414

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Madalitso kazombo kamatcheni posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share