Zochitaka Kwa Nankumba

Zochitaka Kwa  Nankumba Zochitaka Kwa Nanku back

04/05/2022

God is good

08/09/2021

OSADELA NKHAWA NDMAVUTO MULINAWO ALIPO AMENE AMATHESA ZOSEZO YESU KRIST YEKHA BASI MUZENI NLHAWA YANU NDIPO AZAKUTHANDINI NDIPO IYE SALEPHELA NDIOKHULUPILIKA NTHAWI ZOSE AMEN

03/06/2021

Mawu Amalenga: Pamene Tathedwa Zeru Ndmavuto'matenda'nkhaza Nd Uphawi Tisazinenere Mau Osonyeza Kugoja Bible Limat Mau Amalenga Ndlilime Lathu Ndzotheka Kuzinela Mdaliso'machiliso Komas Mtendele Paumoyo Wathu Mzina La Yesu Khrist Ndpo Nyengo Zathu Zizastha Amen

13/11/2020
24/10/2020

Watizusa ndimoyo Mulungu choyamba timuthokozy potizusa ndimoyo watikomera mtima kuliwonaso tsiku lalero

15/10/2020

Gaez kukacha kujaku ndikuzuka ndi Moyo tiyeni tizimuthokoza Mulungu nthawi zonse pozuka chifukwa amatiteteza kuzambili musikuwu!!! Amen

Address

Mangochi

Opening Hours

09:00 - 17:00

Telephone

+265883558361

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Zochitaka Kwa Nankumba posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share