02/11/2025
Kodi ndi bwino kuti mamuna akuchoka ku masewera olimbitsa thupi basi kufika kunyumba nkazache adziti,
“mamuna wanji omangosapota zoluza? Ukungotha ndalama pakhomo pano kumalipira ku Stadium, kodi sumaona amuna anzako odziwa kusankha bwino matimu? Ubwelere ukagone komwe kumagona timu yakoyo!”
Mesa kodi mamuna ndi mwana? My Man kumupanga choncho zoona? Head of the house kumulalatira pakhomo pake pomwe? Kumuyalutsa Hubby pagulu choncho zoona?
Ndibwino?😭😭
Akufunsa ku Max & sherry