Adziwi

Adziwi Sports | Entertainment | News updates

women!!
15/03/2026

women!!

Angokwiyatu zilizonse kuno
15/03/2026

Angokwiyatu zilizonse kuno

15/03/2026

in case you have a bad night

Nde mwati njira imeneyi ikulowera k*t ,sindikumvesesa bwinobwino
15/03/2026

Nde mwati njira imeneyi ikulowera k*t ,sindikumvesesa bwinobwino

Ukhonza kukhalanazo zonse zokuyenereza koma ngat sukuziwa k*t ungagwilise ntchito bwanji, iweyo ndek*t ndichimodzmodz nd...
14/03/2026

Ukhonza kukhalanazo zonse zokuyenereza koma ngat sukuziwa k*t ungagwilise ntchito bwanji, iweyo ndek*t ndichimodzmodz ndi che Yusufu apamtundapo.

14/03/2026

Full-Time ⚽ mpira ukuyenda bwino kwambili

Chelsea 0-1 Newcastle
Arsenal 2-0 Everton

Iran ikufuna kuyamba kulimbanano ndi Ukraine pachifukwa chomwe ak*ti yathandiza Israel ndipo zikuonesa k*t Usiku uno Ukr...
14/03/2026

Iran ikufuna kuyamba kulimbanano ndi Ukraine pachifukwa chomwe ak*ti yathandiza Israel ndipo zikuonesa k*t Usiku uno Ukraine ili pa Target kukupita Bonus kumeneku.

  Osewera mpira wamiyendo wa Team Ya Nyasa Big Bullets yemwe dzina lake ndi Hassan Kajokewapereka offer yakeAkufuna k*ti...
14/03/2026


Osewera mpira wamiyendo wa Team Ya Nyasa Big Bullets yemwe dzina lake ndi Hassan Kajoke
wapereka offer yake
Akufuna k*ti pa mwedzi azilandila ndalama yokwana MK800,000.00

tsono inu Maganizo anu ndiotani pa nkhani imeneyi

WinterCharge ✨️
14/03/2026

WinterCharge ✨️

Nyimbo yatsopano “Kasongo” – A Inno Busy ft Shano Index ikubwera pa 23 March 🔥🎶
14/03/2026

Nyimbo yatsopano “Kasongo” – A Inno Busy ft Shano Index ikubwera pa 23 March 🔥🎶

Address

Chinamwali
Zomba

Telephone

+265881829325

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Adziwi posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share