19/04/2024
Winter nde wabwela kudzakhala kuyendelana kuchepa bibida tidzimwela pakhomo, nde chokhalila pakhomo without entertainment nchani?😏 tiitaneni ife tidzaike dstv,open view kaya yangothawa signal tidzaibwezeletse kuti inu ndapabanja panu musasungulumwe, ana asakuvuteni kufuna ma cartoon chifukwa Choti dstv mnyumba mulibe kapena yathawa alendofe tikabwela mpunga wanyama umakoma kwinaku tikuonela mpira. Gifted hands nde yankho lanu pa mtengo wabwino osaboola mnthumba,
Ubwino wina ndiwakuti, ndiife okambika pa nkhani ya mtengo, Timapeleka guarantee ngati ingathawe pa nthawi tapelekayo tidzidzakonza ulele tiimbileni selula anzanu ayambapo kale.