Blessing Construction and project

Blessing Construction and project Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Blessing Construction and project, Home improvement, 152 Potgieter Avenue, Polokwane.

24/02/2024

Azimayi mumakoma kuposa asikana awa 😂😂😂😂

01/02/2024

😪koma moyo uno olakwa ndiwena olandila chilango ndiwosalakwa 🦷

17/01/2024

😂 kufusilana mu Decembar chaka chantha ndikuvomela mu January pa 17 after alandilodi atalusa 🫵

13/01/2024

Osamazikakamiza chilichose chili ndi nthawi akaziwa ndani kuti iwo azafika pomwe ali 🚪

Naaa maloto awa wina aliyese anadusapo ndipo ena akadalibe kuwalota maka achina yohane 😂😂😂😂
09/01/2024

Naaa maloto awa wina aliyese anadusapo ndipo ena akadalibe kuwalota maka achina yohane 😂😂😂😂

Mwana wa amama anyamwali ndi adada achirwa ndilivi January siku lelosi ndi 25 December 200000000000000 😂😂😂😂😂😂
06/01/2024

Mwana wa amama anyamwali ndi adada achirwa ndilivi January siku lelosi ndi 25 December 200000000000000

😂😂😂😂😂😂

04/01/2024

😂 koma January ada week yoyamba yantha koma kwasalaso ma weeks 4 kuti anthe nde wina ufusile uwone ngati ungakanindwe 🐊

03/01/2024

Avekele 2023 yanthelamo asana pange china chilichose kodi ku toilet ndiku malilo ndikapita kunja inu munali mutangona 🫵

Happy birthday to my young brother happy  I proud of you my man
01/01/2024

Happy birthday to my young brother happy I proud of you my man

31/12/2023

friends and family’s lelo ndipa 31 December 2023 mulungu atikondela tamaliza chakazi bwanji tingoti zikomo ambuye anthu 🙏

Sweet home kugofika last night mamawa uno ndikuyamba kuyendela kaye masala Mumasanamu tikaweze kaye somba pa nkhata bay ...
30/12/2023

Sweet home kugofika last night mamawa uno ndikuyamba kuyendela kaye masala

Mumasanamu tikaweze kaye somba pa nkhata bay ✍️

29/12/2023

😂😂 avekele ine miyendo komaso mutu wa nkhuku sindimadya koma nkhuku ndimadya 👁 nebar uli ndi matama opusa bwanji 🫵

Address

152 Potgieter Avenue
Polokwane
0699

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Blessing Construction and project posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share