Kandodo

Kandodo Nkulemba nthalika zachitonga

Ndikulengezesa business
(1)

06/05/2026

akutelotu akuluwa kumeneko

With little bro
23/02/2026

With little bro

Let there be light...
29/01/2026

Let there be light...

05/01/2026

Story of Night..🀭🀭
Moyo okhala wekha, ulingati ulendo osaziwa komwe ukupita kuti ukasagane naye ndindani....

Tsikulina ndikuchokela ku ntchito, nditatopa ndikupalasa kanjinga kanga... Maganizo alithoo oti ndikafike paden ndikasambe, kenako kayang'ane chakudya....

Ndili Msewu, chifasileni nditasowa mumaganizo mwanga... ndinakumana ndi tsikana wina amapita komwe ine ndimalowela...ndisanamufuse ndinalibe maganizo oyima kuti ndifuse komwe akupita chifukwa ndimamuwopa, mawonekedwe ake anali antengo wapatali....

Ndili busy kupalasa Njinga yanga, tsikana anakuwa ..
Achimwene..!!!!!!
Ine ndinachewuka, tsikana uja anandiyimisa akumwetulira, ineyo kuwona momwe akamwetulilamo ndinati iyi si Level yanga ...

Ndina yima m'mtima ndikuyakhula kuti angonena chomwe afuna ine zipita .. Kenako tsikanq uja avekele chonde ndikufuna tiyende limozi pa bridge apo pamandiwopya...

Nasika njinga yanga
Kuyamba kuyenda wapasi.. Anandifutsa.."

"Kodi zina lako ndiwe ndani ..?"
Ndisanayakhe tibwelerele kaye pambuyo pang'ono.. Kunena za tsikana uyu ..
Anali okongola ndipo mawu oti chiphazuwa, navesesa nditamuwona tsikanayu zoti kulimbee ziyang'ana pamene ndikuponda ndinayamba kumayang'ana tsikanayu... .

Tsikanayu mbuyo ndisayike level mwendo, mabele, ndipo kuzayang'ana milomo ndimene chiphumi chake chinalili anamukoza bwino Mulungu or maso ake amachita kunena zambiri, iyeyo asanayakhule ...

Kenako ndinazayakha "Ine ndi Truth" ndikumupasa zanja kuti ngati zingavute zanja lokha ndingogwila nawo...

Ndinazamuwona akuseka,
"Zina lakodi ndiwe Truth..?
Ndinati "EYA iwe ndi ndani...?"
"Oh ineyo ndi Promise......
Apapatu ineyo ndinali busy ndikuyang'ana mawonekedwe ake zoti akundi yankha ndinalibe nazo ntchito..

Tinayenda Msewu awiri wiri. Paka tinakafika paka town pomwe tinasiyana koma tisana siyane Ndinapempha HUG tsikana anatambasula manja.. ndinataya njinga kumukumbatila tsikanayu, moti anali pafupiwo kaya amati chani ..? ineyo ndimava ngati ndabadwa mwasopano....

Zanja langa straight ku mbuyo kukagwila mbuyo mtima kumati mwina sitizakumanaso.. nthupii langa linatetha, tsikana anandikumbatila bwino ndipo Hag anandipasa tsikanayu sindikuziwa ngati aliposo tsikana amene amatha kupeleka hag ngati imeneyi..

Thupi, linagwidwa ndinyele . magazi anathamanga tsinafune kumusiya koma ndinava ndinthu chinachake mwa iye kuti akufuna tisiyane kenako nazamasula manja anga thawi iyi napempha number
Mtima ndikuti kangoyesa mwina kugwila....

Nditatenga number ndinawona kagalimoto ka Polo, vw. Ka white.. kanafika ndikuzayima straight pamene ife tinali .. Nde munali ada ena akeso owoneka azidola zawo anakuwa nati Promise ..!!! tiye tilibe thawi ... Tsikana ananyamuka kumapita ndi ada ajawo...

Ineyo nditasala ndi fungo la perfume watsikanayu...
Ndinakhala pasi kuti magazi anga akhale mumalo chifukwa ndilindi tsikana uja magazi anayamba kuthamanga, mpaka ine kuyamba kuva kupweteka mumimba chifukwa chomulingalira tsikanayu..
Ma ba***e nde amapweteka nde ndinati ndikhale kaye mwina kusiya....
.....lero tithele p***a towonaso mawa..

19/12/2025

Short story 🫢🫢🌚🌚

Dad : Who do u like more, mum or dad?
Son : Both
Dad : Okay, if I go to Malaysia and your mum goes to Dubai , where will you go?
Son : Dubai
Dad : That shows u love your mum more?
Son : No, it shows i love Dubai more than Malaysia
Dad : Okay, if i go to Dubai and your mum goes to Malaysia , where will u go?
Son : Malaysia
Dad : Replied angrily, why?
Son :🀣🀣🀣🀣why the anger, I chose Malaysia because I have been to Dubai before
Dad : When did you go to Dubai ?
Son : During the first question
πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚

You are laughing right? May joy and laughter never depart from you. πŸ˜‚πŸ˜‚kindly bless me with a reaction

Some photos need to.be  kept i just don't know who will see this but i say hello to you ..!!!
18/12/2025

Some photos need to.be kept
i just don't know who will see this

but i say hello to you ..!!!

03/10/2025

If they don't see your value please just leave

29/08/2025

Osakhala ndi Moyo wa achewa Guys moyo oti ali ndi atumbuka 10 iyeyo osasithako chiyakhulo

27/03/2025

Address

Mzuzu Box 1020
Sandton
1501

Telephone

+27737794743

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Kandodo posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Kandodo:

Share